2 Mbiri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ayuda onse anayamba kusangalala chifukwa analumbira ndi mtima wawo wonse, komanso chifukwa anafunafuna Mulungu mwakhama ndipo iye analola kuti amupeze.+ Ndipo Yehova anapitiriza kuwapatsa mpumulo mʼdziko lonse.+
15 Ayuda onse anayamba kusangalala chifukwa analumbira ndi mtima wawo wonse, komanso chifukwa anafunafuna Mulungu mwakhama ndipo iye analola kuti amupeze.+ Ndipo Yehova anapitiriza kuwapatsa mpumulo mʼdziko lonse.+