2 Mbiri 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma sanachotse malo okwezeka+ mu Isiraeli.+ Ngakhale zinali choncho, Asa anatumikira Mulungu ndi mtima wonse* kwa moyo wake wonse.+
17 Koma sanachotse malo okwezeka+ mu Isiraeli.+ Ngakhale zinali choncho, Asa anatumikira Mulungu ndi mtima wonse* kwa moyo wake wonse.+