2 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mʼchaka cha 36 cha ulamuliro wa Asa, Basa+ mfumu ya Isiraeli anapita kukaukira Yuda ndipo anayamba kumanganso mzinda wa Rama+ kuti ukhale wolimba. Anachita zimenezi kuti anthu asamalowe kapena kutuluka mʼdera la Asa mfumu ya Yuda.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:1 Nsanja ya Olonda,8/15/2012, tsa. 10
16 Mʼchaka cha 36 cha ulamuliro wa Asa, Basa+ mfumu ya Isiraeli anapita kukaukira Yuda ndipo anayamba kumanganso mzinda wa Rama+ kuti ukhale wolimba. Anachita zimenezi kuti anthu asamalowe kapena kutuluka mʼdera la Asa mfumu ya Yuda.+