2 Mbiri 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zitatero, Asa anatenga siliva ndi golide pa chuma chamʼnyumba ya Yehova+ ndi chamʼnyumba ya mfumu nʼkutumiza kwa Beni-hadadi mfumu ya Siriya,+ amene ankakhala ku Damasiko, ndi uthenga wakuti:
2 Zitatero, Asa anatenga siliva ndi golide pa chuma chamʼnyumba ya Yehova+ ndi chamʼnyumba ya mfumu nʼkutumiza kwa Beni-hadadi mfumu ya Siriya,+ amene ankakhala ku Damasiko, ndi uthenga wakuti: