2 Mbiri 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a asilikali ake kuti akamenyane ndi anthu amʼmizinda ya Isiraeli. Iwo analanda Iyoni,+ Dani,+ Abele-maimu ndi malo onse osungiramo zinthu a mʼmizinda ya Nafitali.+
4 Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a asilikali ake kuti akamenyane ndi anthu amʼmizinda ya Isiraeli. Iwo analanda Iyoni,+ Dani,+ Abele-maimu ndi malo onse osungiramo zinthu a mʼmizinda ya Nafitali.+