2 Mbiri 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Basa atamva zimenezi, nthawi yomweyo anasiya kumanga* Rama nʼkuimitsa ntchito yake.