2 Mbiri 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mfumu Asa inatenga Ayuda onse nʼkupita kukatenga miyala ndi matabwa za ku Rama+ zimene Basa ankamangira+ ndipo anakamangira mzinda wa Geba+ ndi wa Mizipa+ kuti mizindayi ikhale yolimba.
6 Ndiyeno Mfumu Asa inatenga Ayuda onse nʼkupita kukatenga miyala ndi matabwa za ku Rama+ zimene Basa ankamangira+ ndipo anakamangira mzinda wa Geba+ ndi wa Mizipa+ kuti mizindayi ikhale yolimba.