2 Mbiri 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi Aitiyopiya ndi Alibiya sanali gulu la asilikali ambiri lokhala ndi magaleta ambiri ndi okwera pamahatchi ambirinso? Koma chifukwa chakuti munadalira Yehova, iye anawapereka mʼmanja mwanu.+
8 Kodi Aitiyopiya ndi Alibiya sanali gulu la asilikali ambiri lokhala ndi magaleta ambiri ndi okwera pamahatchi ambirinso? Koma chifukwa chakuti munadalira Yehova, iye anawapereka mʼmanja mwanu.+