2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maso a Yehova akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake* kwa anthu odzipereka ndi mtima wonse kwa iye.*+ Mwachita zopusa pa nkhani imeneyi. Kuyambira pano mʼdziko lanu muzichitika nkhondo.”+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:9 Yandikirani, tsa. 43 Nsanja ya Olonda,10/15/2002, tsa. 14
9 Maso a Yehova akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake* kwa anthu odzipereka ndi mtima wonse kwa iye.*+ Mwachita zopusa pa nkhani imeneyi. Kuyambira pano mʼdziko lanu muzichitika nkhondo.”+