-
2 Mbiri 16:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho anamuika mʼmanda olemekezeka kwambiri, amene iye anakumbiratu mu Mzinda wa Davide.+ Pomuika mʼmandamo, anamugoneka pachithatha pomwe anathirapo mafuta a basamu ambiri ndi mafuta apadera opangidwa posakaniza zinthu zosiyanasiyana.+ Kuwonjezera pamenepo, pamaliro ake anawotchapo zinthu zambiri zonunkhira.
-