2 Mbiri 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anaika magulu a asilikali mʼmizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Anamanganso midzi ya asilikali ku Yuda ndi mʼmizinda ya Efuraimu imene Asa bambo ake analanda.+
2 Iye anaika magulu a asilikali mʼmizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Anamanganso midzi ya asilikali ku Yuda ndi mʼmizinda ya Efuraimu imene Asa bambo ake analanda.+