2 Mbiri 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anachititsa kuti ufumuwo ukhazikike mʼmanja mwake+ ndipo Ayuda onse ankapereka mphatso kwa Yehosafati. Choncho iye anali ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero wochuluka.+
5 Yehova anachititsa kuti ufumuwo ukhazikike mʼmanja mwake+ ndipo Ayuda onse ankapereka mphatso kwa Yehosafati. Choncho iye anali ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero wochuluka.+