2 Mbiri 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anayamba kuphunzitsa mu Yuda ndipo ankatenga buku la Chilamulo cha Yehova.+ Ankayenda mʼmizinda yonse ya Yuda nʼkumaphunzitsa anthu.
9 Iwo anayamba kuphunzitsa mu Yuda ndipo ankatenga buku la Chilamulo cha Yehova.+ Ankayenda mʼmizinda yonse ya Yuda nʼkumaphunzitsa anthu.