-
2 Mbiri 17:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Afilisiti ankabweretsa mphatso ndi ndalama kwa Yehosafati monga msonkho. Aluya ankamubweretsera ziweto. Ankabweretsa nkhosa zamphongo 7,700 ndi atonde a mbuzi 7,700.
-