2 Mbiri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehosafati anapitiriza kukhala wamphamvu+ ndipo anapitiriza kumanga mipanda yolimba kwambiri+ ndiponso mizinda yosungirako zinthu+ mʼdziko la Yuda.
12 Yehosafati anapitiriza kukhala wamphamvu+ ndipo anapitiriza kumanga mipanda yolimba kwambiri+ ndiponso mizinda yosungirako zinthu+ mʼdziko la Yuda.