2 Mbiri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehosafati anali ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero waukulu,+ koma anachita mgwirizano wa ukwati ndi Ahabu.+
18 Yehosafati anali ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero waukulu,+ koma anachita mgwirizano wa ukwati ndi Ahabu.+