-
2 Mbiri 18:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho mfumu ya Isiraeli inasonkhanitsa aneneri. Analipo amuna 400 ndipo inawafunsa kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi, kapena ndisapite?” Iwo anayankha kuti: “Pitani ndipo Mulungu woona akapereka mzindawo kwa inu mfumu.”
-