2 Mbiri 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Yehosafati anafunsa kuti: “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova?+ Ngati alipo, tiyeni tifunsirenso kwa Mulungu kudzera mwa iyeyo.”+
6 Kenako Yehosafati anafunsa kuti: “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova?+ Ngati alipo, tiyeni tifunsirenso kwa Mulungu kudzera mwa iyeyo.”+