2 Mbiri 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anakhala pabwalo* lapageti lolowera mumzinda wa Samariya. Aliyense anakhala pampando wake wachifumu atavala zovala zachifumu ndipo aneneri onse ankalosera pamaso pawo.
9 Mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anakhala pabwalo* lapageti lolowera mumzinda wa Samariya. Aliyense anakhala pampando wake wachifumu atavala zovala zachifumu ndipo aneneri onse ankalosera pamaso pawo.