-
2 Mbiri 18:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndiyeno Zedekiya mwana wa Kenaana anapanga nyanga zachitsulo nʼkunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndi nyanga izi mudzagunda Asiriya mpaka kuwapha onse.’”
-