-
2 Mbiri 18:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako anafika kwa mfumu ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Mikaya, kodi tipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi kapena tisapite?” Nthawi yomweyo Mikaya anayankha kuti: “Pitani mukapambana ndipo mzindawo ukaperekedwa kwa inu mfumu.”
-