2 Mbiri 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika mʼmapiri ngati nkhosa zopanda mʼbusa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe mtsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mwamtendere.’”
16 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika mʼmapiri ngati nkhosa zopanda mʼbusa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe mtsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mwamtendere.’”