2 Mbiri 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba+ linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+
18 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba+ linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+