-
2 Mbiri 18:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu mfumu ya Isiraeli, kuti apite ku Ramoti-giliyadi nʼkukafa?’ Choncho angelo osiyanasiyana ankanena maganizo awo, wina izi, wina izi.
-