-
2 Mbiri 18:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Ine ndidzisintha kuti ndisadziwike ndipo ndimenya nawo nkhondo. Koma inuyo muvale zovala zanu zachifumu.” Choncho mfumu ya Isiraeli inadzisintha nʼkuyamba kumenya nawo nkhondo.
-