-
2 Mbiri 18:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu oyangʼanira asilikali okwera magaleta kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamngʼono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”
-