2 Mbiri 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo ndipo mfumuyo anaiimiritsa mʼgaleta nʼkuitsamiritsa kugaletalo moyangʼanizana ndi Asiriya mpaka madzulo. Mfumuyo inafa pamene dzuwa linkalowa.+
34 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo ndipo mfumuyo anaiimiritsa mʼgaleta nʼkuitsamiritsa kugaletalo moyangʼanizana ndi Asiriya mpaka madzulo. Mfumuyo inafa pamene dzuwa linkalowa.+