2 Mbiri 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya, anapita kwa Mfumu Yehosafati ndipo anamufunsa kuti: “Kodi muyenera kuthandiza anthu oipa,+ ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2021, tsa. 3
2 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya, anapita kwa Mfumu Yehosafati ndipo anamufunsa kuti: “Kodi muyenera kuthandiza anthu oipa,+ ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani.