2 Mbiri 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehosafati anapitiriza kukhala ku Yerusalemu. Iye anapitanso kwa anthu, kuyambira ku Beere-seba mpaka kudera lamapiri la Efuraimu,+ kuti awabwezere kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.+
4 Yehosafati anapitiriza kukhala ku Yerusalemu. Iye anapitanso kwa anthu, kuyambira ku Beere-seba mpaka kudera lamapiri la Efuraimu,+ kuti awabwezere kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.+