2 Mbiri 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaikanso oweruza mʼdziko lonselo, mumzinda ndi mzinda, ndipo anachita zimenezi mʼmizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
5 Anaikanso oweruza mʼdziko lonselo, mumzinda ndi mzinda, ndipo anachita zimenezi mʼmizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+