2 Mbiri 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena, ansembe ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo a Isiraeli, kuti akhale oweruza mʼmalo mwa Yehova ndipo aziweruza milandu ya anthu a ku Yerusalemu.+
8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena, ansembe ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo a Isiraeli, kuti akhale oweruza mʼmalo mwa Yehova ndipo aziweruza milandu ya anthu a ku Yerusalemu.+