-
2 Mbiri 19:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Abale anu, amene akukhala mʼmizinda yawo, akabwera ndi mlandu wokhudza kukhetsa magazi+ komanso funso lokhudza malamulo kapena ziweruzo, muziwachenjeza kuti asalakwire Yehova kuopera kuti Mulungu angakukwiyireni kwambiri inuyo ndiponso abale anuwo. Muzichita zimenezi nʼcholinga choti musapalamule mlandu.
-