2 Mbiri 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Amowabu,+ Aamoni+ ndi Aamonimu* ena anabwera kudzamenyana ndi Yehosafati.