2 Mbiri 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 nʼkunena kuti: “Inu Yehova Mulungu wa makolo athu, kodi si inu Mulungu wakumwamba?+ Kodi inu simukulamulira maufumu onse a mitundu ya anthu?+ Mʼdzanja lanu muli mphamvu ndipo palibe amene angalimbane nanu.+
6 nʼkunena kuti: “Inu Yehova Mulungu wa makolo athu, kodi si inu Mulungu wakumwamba?+ Kodi inu simukulamulira maufumu onse a mitundu ya anthu?+ Mʼdzanja lanu muli mphamvu ndipo palibe amene angalimbane nanu.+