2 Mbiri 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu wathu, kodi si paja munathamangitsa anthu amene ankakhala mʼdzikoli pamaso pa anthu anu Aisiraeli nʼkulipereka kwa mbadwa* za Abulahamu, bwenzi lanu, kuti likhale lawo mpaka kalekale?+
7 Inu Mulungu wathu, kodi si paja munathamangitsa anthu amene ankakhala mʼdzikoli pamaso pa anthu anu Aisiraeli nʼkulipereka kwa mbadwa* za Abulahamu, bwenzi lanu, kuti likhale lawo mpaka kalekale?+