2 Mbiri 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Tsoka likatigwera, kaya lupanga, chiweruzo chowawa, mliri kapena njala, tiziima patsogolo pa nyumbayi ndi pamaso panu (popeza dzina lanu lili mʼnyumbayi)+ nʼkufuulira inu kuti mutithandize pa mavuto athu, ndipo inu muzitimva nʼkutipulumutsa.’+
9 ‘Tsoka likatigwera, kaya lupanga, chiweruzo chowawa, mliri kapena njala, tiziima patsogolo pa nyumbayi ndi pamaso panu (popeza dzina lanu lili mʼnyumbayi)+ nʼkufuulira inu kuti mutithandize pa mavuto athu, ndipo inu muzitimva nʼkutipulumutsa.’+