2 Mbiri 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Aamoni, Amowabu ndi anthu akudera lamapiri la Seiri+ abwera. Inu simunalole kuti Aisiraeli alowe mʼdziko lawo pamene ankachokera ku Iguputo ndipo sanawaphe.+
10 Tsopano Aamoni, Amowabu ndi anthu akudera lamapiri la Seiri+ abwera. Inu simunalole kuti Aisiraeli alowe mʼdziko lawo pamene ankachokera ku Iguputo ndipo sanawaphe.+