2 Mbiri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi gulu lalikulu limene likudzamenyana nafeli ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+
12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi gulu lalikulu limene likudzamenyana nafeli ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+