-
2 Mbiri 20:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mawa mupite kukakumana nawo. Iwo adzabwera kudzera pampata wa Zizi. Mudzawapeza kumapeto kwa chigwa musanafike kuchipululu cha Yerueli.
-