2 Mbiri 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo. Aliyense angoima pamalo ake+ nʼkuona mmene Yehova angakupulumutsireni.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:17 Nkhani za M’Baibulo, ptsa. 120-121 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, tsa. 216/1/2003, ptsa. 21-22
17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo. Aliyense angoima pamalo ake+ nʼkuona mmene Yehova angakupulumutsireni.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+