-
2 Mbiri 20:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Nthawi yomweyo Yehosafati anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi, ndipo Ayuda onse ndi anthu a ku Yerusalemu anawerama pamaso pa Yehova kuti alambire Yehovayo.
-