2 Mbiri 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aamoni ndi Amowabu anaukira anthu okhala kudera lamapiri la Seiri+ ndipo anayamba kuwapha mpaka kuwamaliza. Atatha kupha anthu a ku Seiri, iwo anaphana okhaokha.+
23 Aamoni ndi Amowabu anaukira anthu okhala kudera lamapiri la Seiri+ ndipo anayamba kuwapha mpaka kuwamaliza. Atatha kupha anthu a ku Seiri, iwo anaphana okhaokha.+