2 Mbiri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa tsiku la 4 anasonkhana kuchigwa cha Beraka ndipo anatamanda* Yehova kumeneko. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti chigwa cha Beraka*+ mpaka lero.
26 Pa tsiku la 4 anasonkhana kuchigwa cha Beraka ndipo anatamanda* Yehova kumeneko. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti chigwa cha Beraka*+ mpaka lero.