2 Mbiri 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehosafati anapitiriza kulamulira ku Yuda. Iye anali ndi zaka 35 pamene ankakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba mwana wa Sili.+
31 Yehosafati anapitiriza kulamulira ku Yuda. Iye anali ndi zaka 35 pamene ankakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba mwana wa Sili.+