2 Mbiri 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komabe sanachotse malo okwezeka+ ndipo anthu anali asanakonze mitima yawo kuti atsatire Mulungu wa makolo awo.+
33 Komabe sanachotse malo okwezeka+ ndipo anthu anali asanakonze mitima yawo kuti atsatire Mulungu wa makolo awo.+