2 Mbiri 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nkhani zina zokhudza Yehosafati, kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene Yehu+ mwana wa Haneni+ analemba ndipo zinaphatikizidwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:34 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 32
34 Nkhani zina zokhudza Yehosafati, kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene Yehu+ mwana wa Haneni+ analemba ndipo zinaphatikizidwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli.