2 Mbiri 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Eliezere mwana wa Dodavahu wa ku Maresa analosera zinthu zotsutsana ndi Yehosafati kuti: “Chifukwa chakuti mwachita mgwirizano ndi Ahaziya, Yehova awononga ntchito yanu.”+ Choncho zombozo zinasweka+ ndipo sizinathenso kupita ku Tarisi.
37 Koma Eliezere mwana wa Dodavahu wa ku Maresa analosera zinthu zotsutsana ndi Yehosafati kuti: “Chifukwa chakuti mwachita mgwirizano ndi Ahaziya, Yehova awononga ntchito yanu.”+ Choncho zombozo zinasweka+ ndipo sizinathenso kupita ku Tarisi.