2 Mbiri 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Yehosafati, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide. Ndiyeno mwana wake Yehoramu anakhala mfumu mʼmalo mwake.+
21 Kenako Yehosafati, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide. Ndiyeno mwana wake Yehoramu anakhala mfumu mʼmalo mwake.+