2 Mbiri 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Bambo awo anawapatsa mphatso zambiri zasiliva ndi zagolide, zinthu zina zamtengo wapatali komanso mizinda ya ku Yuda+ yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Koma ufumu anaupereka kwa Yehoramu+ chifukwa ndi amene anali woyamba kubadwa.
3 Bambo awo anawapatsa mphatso zambiri zasiliva ndi zagolide, zinthu zina zamtengo wapatali komanso mizinda ya ku Yuda+ yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Koma ufumu anaupereka kwa Yehoramu+ chifukwa ndi amene anali woyamba kubadwa.