2 Mbiri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, anapha ndi lupanga azichimwene ake onse+ ndiponso akalonga ena a Isiraeli. Iye anachita zimenezi kuti alimbitse ufumu wake.
4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, anapha ndi lupanga azichimwene ake onse+ ndiponso akalonga ena a Isiraeli. Iye anachita zimenezi kuti alimbitse ufumu wake.